Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 274
10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+