Yohane 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma tsopano ndikubwera kwa inu, ndipo ndikulankhula zimenezi pamene ndili m’dziko kuti akhale ndi chimwemwe chosefukira ngati chimene ine ndili nacho.+
13 Koma tsopano ndikubwera kwa inu, ndipo ndikulankhula zimenezi pamene ndili m’dziko kuti akhale ndi chimwemwe chosefukira ngati chimene ine ndili nacho.+