Yohane 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Petulo anaimirira kunja pakhomo.+ Choncho wophunzira winayu, amene anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe uja, anapita kukalankhula ndi mlonda wa pakhomo ndipo analowetsa Petulo. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:16 Buku la Onse, ptsa. 16-17 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
16 Koma Petulo anaimirira kunja pakhomo.+ Choncho wophunzira winayu, amene anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe uja, anapita kukalankhula ndi mlonda wa pakhomo ndipo analowetsa Petulo.