Yohane 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:22 Nsanja ya Olonda,4/1/2011, tsa. 19
22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”