Yohane 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:25 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+