Yohane 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zimenezi zitatha, Yesu anaonekeranso kwa ophunzirawo kunyanja ya Tiberiyo.* Kuonekera kwakeko kunali motere.
21 Zimenezi zitatha, Yesu anaonekeranso kwa ophunzirawo kunyanja ya Tiberiyo.* Kuonekera kwakeko kunali motere.