Yohane 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atanena choncho, mawu amenewa anafalikira mwa abale, kuti wophunzira ameneyu sadzamwalira. Koma Yesu sanamuuze kuti sadzamwalira, koma ananena kuti: “Ngati ine nditafuna kuti akhalebe+ kufikira ndikadzabwera, kodi iwe uli nazo kanthu?”
23 Atanena choncho, mawu amenewa anafalikira mwa abale, kuti wophunzira ameneyu sadzamwalira. Koma Yesu sanamuuze kuti sadzamwalira, koma ananena kuti: “Ngati ine nditafuna kuti akhalebe+ kufikira ndikadzabwera, kodi iwe uli nazo kanthu?”