Machitidwe 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene iye anali pa msonkhano limodzi ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musatuluke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere chimene Atate analonjeza,+ chimene munamva kwa ine.
4 Pamene iye anali pa msonkhano limodzi ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musatuluke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere chimene Atate analonjeza,+ chimene munamva kwa ine.