Machitidwe 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:26 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 19 Yesu—Ndi Njira, tsa. 311 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 11
26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.