Machitidwe 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzidzidzi kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo unadzaza m’nyumba yonse imene iwo anakhalamo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 21 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 13-146/1/1990, ptsa. 11-12
2 Mwadzidzidzi kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo unadzaza m’nyumba yonse imene iwo anakhalamo.+