Machitidwe 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anaona malawi amoto ooneka ngati malilime,+ ndipo anagawanika ndi kukhala pa aliyense wa iwo limodzilimodzi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 21 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 13-14
3 Pamenepo anaona malawi amoto ooneka ngati malilime,+ ndipo anagawanika ndi kukhala pa aliyense wa iwo limodzilimodzi.