Machitidwe 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawiyo mu Yerusalemu munali kukhala Ayuda ena,+ anthu oopa Mulungu,+ ochokera mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,12/1/2015, tsa. 113/15/1989, tsa. 25 Yesaya 2, tsa. 408
5 Pa nthawiyo mu Yerusalemu munali kukhala Ayuda ena,+ anthu oopa Mulungu,+ ochokera mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo.