Machitidwe 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yesu ameneyo Mulungu anamuukitsa, ndipo tonsefe ndife mboni za choonadi chimenecho.+