Machitidwe 2:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+
43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+