Machitidwe 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 28
7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+