Machitidwe 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Petulo ataona zimenezi, anauza anthuwo kuti: “Aisiraeli inu, n’chifukwa chiyani mukudabwa nazo zimenezi? N’chifukwa chiyani mukutiyang’anitsitsa ngati kuti tamuyendetsa mwa mphamvu zathu, kapena chifukwa cha kudzipereka kwathu kwa Mulungu?+
12 Petulo ataona zimenezi, anauza anthuwo kuti: “Aisiraeli inu, n’chifukwa chiyani mukudabwa nazo zimenezi? N’chifukwa chiyani mukutiyang’anitsitsa ngati kuti tamuyendetsa mwa mphamvu zathu, kapena chifukwa cha kudzipereka kwathu kwa Mulungu?+