Machitidwe 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo aneneri onse, kuyambira pa Samueli mpaka aneneri onse amene anabwera m’mbuyo mwake, onse amene analosera, ananena mosapita m’mbali za masiku amenewa.+
24 Ndipo aneneri onse, kuyambira pa Samueli mpaka aneneri onse amene anabwera m’mbuyo mwake, onse amene analosera, ananena mosapita m’mbali za masiku amenewa.+