Machitidwe 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yesu ameneyu ndiye ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, ptsa. 12-137/15/2000, tsa. 14
11 Yesu ameneyu ndiye ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+