Machitidwe 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, panalibe ndi mmodzi yemwe mwa enawo amene analimba mtima kuphatikana ndi ophunzirawo,+ koma anthu anali kuwatamanda.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 14
13 Ndithudi, panalibe ndi mmodzi yemwe mwa enawo amene analimba mtima kuphatikana ndi ophunzirawo,+ koma anthu anali kuwatamanda.+