Machitidwe 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Pitani, ndipo mukaimirire m’kachisi ndi kupitiriza kuuza anthu zoyenera kuchita kuti adzapeze moyo umene ukubwerawo.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 38
20 “Pitani, ndipo mukaimirire m’kachisi ndi kupitiriza kuuza anthu zoyenera kuchita kuti adzapeze moyo umene ukubwerawo.”+