Machitidwe 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako kunali Yudasi Mgalileya m’masiku a kalembera.+ Iyeyu anakopa anthu ndipo anamutsatira. Koma munthu ameneyunso anafa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalikabalalika. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:37 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 6 Galamukani!,9/8/1987, tsa. 8
37 Kenako kunali Yudasi Mgalileya m’masiku a kalembera.+ Iyeyu anakopa anthu ndipo anamutsatira. Koma munthu ameneyunso anafa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalikabalalika.