Machitidwe 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+
5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+