Machitidwe 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Chotero anabereka Isaki+ ndi kuchita mdulidwe wake tsiku la 8.+ Isaki naye anabereka Yakobo, Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.+
8 “Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Chotero anabereka Isaki+ ndi kuchita mdulidwe wake tsiku la 8.+ Isaki naye anabereka Yakobo, Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.+