Machitidwe 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mose anali kuganiza kuti abale akewo azindikira kuti Mulungu akuwapatsa chipulumutso kudzera m’dzanja lake,+ koma iwo sanaizindikire mfundo imeneyi.
25 Mose anali kuganiza kuti abale akewo azindikira kuti Mulungu akuwapatsa chipulumutso kudzera m’dzanja lake,+ koma iwo sanaizindikire mfundo imeneyi.