Machitidwe 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+
26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+