Machitidwe 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova anamuuza kuti, ‘Vula nsapato zako, pakuti malo amene waimawo ndi malo oyera.+