42 Chotero Mulungu anawaleka+ kuti atumikire makamu akumwamba monga mmene malemba amanenera m’buku la aneneri.+ Malembawo amati, ‘Anthu inu a nyumba ya Isiraeli, kodi m’chipululu muja munali kupereka kwa ine nyama zansembe ndi zopereka zina kwa zaka 40?+