Machitidwe 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Amuna inu, abale anga, inu ana a mbadwa za Abulahamu, ndi ena onse oopa Mulungu amene ali pakati panu, mawu a chipulumutso chimenechi atumizidwa kwa ife.+
26 “Amuna inu, abale anga, inu ana a mbadwa za Abulahamu, ndi ena onse oopa Mulungu amene ali pakati panu, mawu a chipulumutso chimenechi atumizidwa kwa ife.+