Machitidwe 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:32 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 147 Nsanja ya Olonda,7/15/2010, tsa. 317/1/1998, tsa. 12
32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”