Machitidwe 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena, Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160
19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena,