Machitidwe 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Izi zinadziwika kwa onse, Ayuda ndi Agiriki amene anali kukhala ku Efeso. Chotero onse anagwidwa ndi mantha,+ ndipo dzina la Ambuye Yesu linapitirira kulemekezedwa.+
17 Izi zinadziwika kwa onse, Ayuda ndi Agiriki amene anali kukhala ku Efeso. Chotero onse anagwidwa ndi mantha,+ ndipo dzina la Ambuye Yesu linapitirira kulemekezedwa.+