-
Machitidwe 19:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndipo chimene chikuopsa kwambiri si kunyozeka kwa ntchito yathu kokha ayi, komanso kachisi wa mulungu wamkulu wamkazi Atemi+ adzayesedwa wopanda pake. Ndipotu aliyense m’chigawo chonse cha Asia komanso padziko lapansi kumene kuli anthu amalemekeza Atemi. Koma chifukwa cha zimene Paulo akunena ulemerero umenewo watsala pang’ono kuti utheretu.”
-