35 Pamapeto pake, woyang’anira mzinda atakhalitsa chete+ khamu la anthulo, anati: “Anthu inu a mu Efeso, alipo kodi munthu amene sadziwa kuti mzinda wa Aefeso ndiwo woyang’anira kachisi wa Atemi wamkulu ndi chifaniziro chimene chinagwa kuchokera kumwamba?