Machitidwe 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chipinda cham’mwamba+ mmene tinasonkhanamo, munali nyale zambiri ndithu. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:8 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 165