-
Machitidwe 20:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Atatero Paulo anakweranso m’chipinda cham’mwamba chija. Kenako ananyemanyema mkate n’kuyamba kudya, ndipo atakambirana kwa nthawi yaitali mpaka m’mawa, ananyamuka n’kumapita.
-