Machitidwe 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Atanena zimenezi, anagwada+ nawo pansi onsewo ndi kupemphera.