Aroma 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ndine Paulo kapolo+ wa Yesu Khristu, woitanidwa+ kuti ndikhale mtumwi,+ ndiponso wosankhidwa kuti ndilalikire uthenga wabwino wa Mulungu.+
1 Ndine Paulo kapolo+ wa Yesu Khristu, woitanidwa+ kuti ndikhale mtumwi,+ ndiponso wosankhidwa kuti ndilalikire uthenga wabwino wa Mulungu.+