Aroma 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choyamba, ndikuyamika+ Mulungu wanga kudzera mwa Yesu Khristu chifukwa cha nonsenu, pakuti chikhulupiriro chanu chikusimbidwa+ m’dziko lonse.
8 Choyamba, ndikuyamika+ Mulungu wanga kudzera mwa Yesu Khristu chifukwa cha nonsenu, pakuti chikhulupiriro chanu chikusimbidwa+ m’dziko lonse.