Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Utumiki wa Ufumu,12/1995, Nsanja ya Olonda,1/1/1990, ptsa. 10-152/1/1987, tsa. 23
16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+