Aroma 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma chifukwa cha lonjezo+ la Mulungu, iye sanagwedezeke pa chikhulupiriro chake+ ndipo chikhulupiriro chakecho chinamulimbitsa.+ Mwa kutero, anapereka ulemerero kwa Mulungu Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:20 Nsanja ya Olonda,7/1/2001, tsa. 21
20 Koma chifukwa cha lonjezo+ la Mulungu, iye sanagwedezeke pa chikhulupiriro chake+ ndipo chikhulupiriro chakecho chinamulimbitsa.+ Mwa kutero, anapereka ulemerero kwa Mulungu