Aroma 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa pamene tinali kukhala mogwirizana ndi thupi,+ zilakolako za uchimo zimene zinaonekera chifukwa cha Chilamulo zinali kugwira ntchito m’ziwalo zathu kuti tibale zipatso za imfa.+
5 Chifukwa pamene tinali kukhala mogwirizana ndi thupi,+ zilakolako za uchimo zimene zinaonekera chifukwa cha Chilamulo zinali kugwira ntchito m’ziwalo zathu kuti tibale zipatso za imfa.+