Aroma 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma chifukwa cha lamulo,+ uchimo unapeza njira yondichititsa kukhala wosirira chinthu chilichonse mwansanje. Chifukwa popanda chilamulo, uchimo unali wakufa.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Nsanja ya Olonda,6/15/2008, tsa. 30
8 Koma chifukwa cha lamulo,+ uchimo unapeza njira yondichititsa kukhala wosirira chinthu chilichonse mwansanje. Chifukwa popanda chilamulo, uchimo unali wakufa.+