Aroma 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma tsopano amene akuchita zimenezo si inenso ayi, koma uchimo umene uli mwa ine.+