Aroma 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu adzatero kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.+ Chotero, m’maganizo mwanga ineyo ndine kapolo wa chilamulo cha Mulungu,+ koma m’thupi langa ndine kapolo wa chilamulo cha uchimo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2017, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,12/1/1997, tsa. 11
25 Mulungu adzatero kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.+ Chotero, m’maganizo mwanga ineyo ndine kapolo wa chilamulo cha Mulungu,+ koma m’thupi langa ndine kapolo wa chilamulo cha uchimo.+