Aroma 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, ptsa. 11-12
3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi.