Aroma 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu.
9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu.