Aroma 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukapha zochita za thupi+ mwa mzimu, mudzakhala ndi moyo.
13 Pakuti ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukapha zochita za thupi+ mwa mzimu, mudzakhala ndi moyo.