Aroma 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti monga mmene inuyo munalili osamvera+ Mulungu koma tsopano mwasonyezedwa chifundo+ chifukwa cha kusamvera kwawo,+
30 Pakuti monga mmene inuyo munalili osamvera+ Mulungu koma tsopano mwasonyezedwa chifundo+ chifukwa cha kusamvera kwawo,+