Aroma 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amene amasunga tsiku amalisungira kulemekeza Yehova. Amene amadya, amadya kuti alemekeze Yehova,+ chifukwa amayamika Mulungu.+ Amene sadya, sadya pofuna kulemekeza Yehova,+ chifukwa nayenso amayamika Mulungu.+
6 Amene amasunga tsiku amalisungira kulemekeza Yehova. Amene amadya, amadya kuti alemekeze Yehova,+ chifukwa amayamika Mulungu.+ Amene sadya, sadya pofuna kulemekeza Yehova,+ chifukwa nayenso amayamika Mulungu.+