Aroma 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma tsopano popeza kulibenso gawo limene sindinafikeko m’madera amenewa, ndiponso popeza kuti kwa zaka zambiri ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko,+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2020, ptsa. 16-17
23 Koma tsopano popeza kulibenso gawo limene sindinafikeko m’madera amenewa, ndiponso popeza kuti kwa zaka zambiri ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko,+